Bible Bard

Cicē'ōẏā_BB-75_Za Mdyerekezi

Informações:

Synopsis

Monga mabuku, Baibulo limafotokoza nkhani zambiri. Pamene tinayang'ana pa maina omwe amagwiritsira ntchito kwa Mulungu tinapeza kuti zambiri za makhalidwe a Mulungu zimawululidwa ndi maina ake (onani BB-68 Maina a Mulungu). Nkhaniyi ikufotokoza za kumene Baibulo limanena kuti mdyerekezi anachokera komanso kuti kutsutsa kwake Mulungu kunakhalako bwanji.